Salimo 73:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, anthu amenewa ali ngati maloto amene aiwalika podzuka.+Choncho pamene mukuimirira mudzawakana mochititsa manyazi.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 73:20 Nsanja ya Olonda,7/15/1993, ptsa. 29-30
20 Inu Yehova, anthu amenewa ali ngati maloto amene aiwalika podzuka.+Choncho pamene mukuimirira mudzawakana mochititsa manyazi.+