Salimo 73:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 73:22 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 127/15/1993, tsa. 30
22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+