Salimo 79:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 79:9 Nsanja ya Olonda,7/15/2006, tsa. 12
9 Tithandizeni inu Mulungu wa chipulumutso chathu,+Kuti dzina lanu lilemekezedwe.+Tipulumutseni ndi kutikhululukira* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+