Salimo 81:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti limeneli ndi lamulo kwa Isiraeli,+Komanso chigamulo cha Mulungu wa Yakobo.