Salimo 81:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mulungu akuti: “Ndinachotsa goli paphewa lake.+Manja ake anamasuka ndipo sananyamule dengu.+