Salimo 83:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Asuri nawonso agwirizana nawo,+Ndipo amapereka thandizo kwa ana aamuna a Loti.+ [Seʹlah.]