Salimo 83:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anena kuti: “Tiyeni tilande malo amene Mulungu amakhalako kuti akhale athu.”+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 83:12 Nsanja ya Olonda,10/15/2008, ptsa. 13-14