Salimo 96:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 96:3 Nsanja ya Olonda,4/15/2001, tsa. 8
3 Lengezani ulemerero wake pakati pa anthu a mitundu ina,+Ndiponso ntchito zake zodabwitsa pakati pa mitundu yonse ya anthu.+