Salimo 96:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova ndi wamkulu+ ndi woyenera kutamandidwa kwambiri.Iye ndi wochititsa mantha kuposa milungu ina yonse.+
4 Pakuti Yehova ndi wamkulu+ ndi woyenera kutamandidwa kwambiri.Iye ndi wochititsa mantha kuposa milungu ina yonse.+