Salimo 97:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kumwamba kwalengeza za chilungamo chake,+Ndipo mitundu yonse ya anthu yaona ulemerero wake.+