Salimo 97:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 97:7 Nsanja ya Olonda,1/15/1992, tsa. 23
7 Onse amene akupembedza chifaniziro chilichonse achite manyazi.+Amene amadzitama chifukwa cha milungu yopanda pake achite manyazi.+Muweramireni, inu milungu yonse.+