Salimo 102:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 102 Inu Yehova, imvani pemphero langa.+Imvani kufuula kwanga kopempha thandizo.+