Salimo 103:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wachifundo ndi wachisomo,+Wosakwiya msanga ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+