Salimo 103:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tamandani Yehova inu makamu ake onse,+Inu atumiki ake onse ochita chifuniro chake.+