Salimo 109:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+
16 Chifukwa chakuti sanakumbukire kusonyeza kukoma mtima kosatha,+M’malomwake anapitiriza kuthamangitsa wosautsika ndi wosauka,+Komanso munthu wa mtima wachisoni kuti amuphe.+