Salimo 109:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma inu ndinu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndikomereni mtima chifukwa cha dzina lanu.+Ndilanditseni,+ popeza kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwakukulu.
21 Koma inu ndinu Yehova Ambuye Wamkulu Koposa.+Ndikomereni mtima chifukwa cha dzina lanu.+Ndilanditseni,+ popeza kukoma mtima kwanu kosatha ndi kwakukulu.