Salimo 119:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndimakondwera kuyenda m’njira ya zikumbutso zanu,+Ngati mmene anthu amachitira akapeza chuma chilichonse chamtengo wapatali.+
14 Ndimakondwera kuyenda m’njira ya zikumbutso zanu,+Ngati mmene anthu amachitira akapeza chuma chilichonse chamtengo wapatali.+