Salimo 119:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Akalonga asonkhana pamodzi kuti akambirane zondiukira.+Koma ine mtumiki wanu, ndimasinkhasinkha malangizo anu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:23 Nsanja ya Olonda,7/15/1997, tsa. 15
23 Akalonga asonkhana pamodzi kuti akambirane zondiukira.+Koma ine mtumiki wanu, ndimasinkhasinkha malangizo anu.+