Salimo 119:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndilangizeni inu Yehova, kuti ndiyende motsatira malangizo anu,+Kuti nditsatire malangizo anu moyo wanga wonse.+
33 Ndilangizeni inu Yehova, kuti ndiyende motsatira malangizo anu,+Kuti nditsatire malangizo anu moyo wanga wonse.+