Salimo 119:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndithandizeni kuti mtima wanga uziganizira zikumbutso zanu,+Osati kupeza phindu.*+