Salimo 119:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndidzayenda uku ndi uku m’malo otakasuka,+Chifukwa ndaphunzira malamulo anu ndi kuwasunga.+