Salimo 119:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+
49 Kumbukirani mawu amene munandiuza ine mtumiki wanu,+Mawu amene ndikuwayembekezera malinga ndi lonjezo lanu.+