Salimo 119:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Anthu odzikuza andinyoza koopsa.+Koma ine sindinapatuke pa chilamulo chanu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:51 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, ptsa. 13-14