Salimo 119:59 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 59 Ndaganizira mozama za njira zanga,+Kuti mapazi anga ndiwabwezere ku zikumbutso zanu.+