Salimo 119:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Pakati pa usiku ndimadzuka kuti ndikuyamikeni+Chifukwa cha zigamulo zanu zolungama.+