Salimo 119:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Inu Yehova, mwandichitiradi zabwino ine mtumiki wanu,+Monga mwa mawu anu.+