Salimo 119:67 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 67 Ndisanagwe m’masautso ndinali kuchimwa mosadziwa,+Koma tsopano ndimasunga mawu anu.+