Salimo 119:78 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 78 Odzikuza achite manyazi, chifukwa andisocheretsa popanda chifukwa,+Koma ine ndimasinkhasinkha malamulo anu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:78 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, ptsa. 14-15
78 Odzikuza achite manyazi, chifukwa andisocheretsa popanda chifukwa,+Koma ine ndimasinkhasinkha malamulo anu.+