Salimo 119:91 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 91 Chilengedwe chonse chakhalapobe kufikira lero chifukwa cha zigamulo zanu,+Pakuti chilengedwe chonse chimakutumikirani.+
91 Chilengedwe chonse chakhalapobe kufikira lero chifukwa cha zigamulo zanu,+Pakuti chilengedwe chonse chimakutumikirani.+