Salimo 119:94 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 94 Ine ndine wanu. Chonde ndipulumutseni,+Chifukwa ndaphunzira malamulo anu ndi kuwasunga.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 119:94 Nsanja ya Olonda,4/15/2005, tsa. 16