Salimo 119:101 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 101 Ndaletsa mapazi anga kuyenda m’njira iliyonse yoipa.+Ndachita izi kuti ndisunge mawu anu.+