Salimo 119:111 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+
111 Ndatenga zikumbutso zanu kukhala chuma changa mpaka kalekale,+Pakuti zimakondweretsa mtima wanga.+