Salimo 119:113 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 113 Ndimadana ndi anthu amitima iwiri,+Koma ndimakonda chilamulo chanu.+