Salimo 119:116 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 116 Inu Mulungu, ndithandizeni monga mwa mawu anu kuti ndikhalebe ndi moyo,+Ndipo musandichititse manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.+
116 Inu Mulungu, ndithandizeni monga mwa mawu anu kuti ndikhalebe ndi moyo,+Ndipo musandichititse manyazi chifukwa cha chiyembekezo changa.+