Salimo 119:154 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 154 Ndiyankhireni mlandu wanga ndi kundipulumutsa.+Ndisungeni wamoyo mogwirizana ndi mawu anu.+