Salimo 119:157 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 157 Anthu ondizunza komanso adani anga ndi ambiri.+Koma ine sindinapatuke pa zikumbutso zanu.+