Salimo 119:158 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 158 Ndaona anthu ochita zinthu mwachinyengo,+Ndipo amandinyansa chifukwa sasunga mawu anu.+