Salimo 119:162 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 162 Ndikukondwera chifukwa cha mawu anu,+Monga mmene munthu amachitira akapeza zofunkha zambiri.+