Salimo 119:163 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 163 Ndimadana ndi chinyengo+ ndipo chimandinyansa,+Koma ndimakonda chilamulo chanu.+