Salimo 129:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Umene wokolola sanadzaze nawo manja ake,+Ngakhalenso aliyense amene akunyamula mitolo ya zokolola sanadzaze nawo thumba lake la pachifuwa.
7 Umene wokolola sanadzaze nawo manja ake,+Ngakhalenso aliyense amene akunyamula mitolo ya zokolola sanadzaze nawo thumba lake la pachifuwa.