Salimo 141:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 141 Inu Yehova, ine ndakuitanani.+Bwerani kwa ine mofulumira.+Tcherani khutu pamene ndikukuitanani.+