Salimo 143:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 143:8 Nsanja ya Olonda,1/15/2010, tsa. 2112/15/1996, tsa. 13
8 M’mawa ndichititseni kumva za kukoma mtima kwanu kosatha,+Pakuti ndimadalira inu.+Ndidziwitseni njira imene ndiyenera kuyendamo,+Pakuti ndapereka moyo wanga kwa inu.+