Salimo 144:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+
2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+