Salimo 144:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amene amalankhula zinthu zonama,+Amenenso dzanja lawo lamanja limachita zachinyengo.+