Salimo 149:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 149 Tamandani Ya, anthu inu!+Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Muimbireni nyimbo zomutamanda mu mpingo wa anthu ake okhulupirika.+
149 Tamandani Ya, anthu inu!+Imbirani Yehova nyimbo yatsopano,+Muimbireni nyimbo zomutamanda mu mpingo wa anthu ake okhulupirika.+