Miyambo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 zimene mumaopa zikadzabwera ngati mvula yamkuntho, tsoka likadzakufikirani ngati mphepo yamkuntho,+ ndiponso masautso ndi nthawi zovuta zikadzakugwerani.+
27 zimene mumaopa zikadzabwera ngati mvula yamkuntho, tsoka likadzakufikirani ngati mphepo yamkuntho,+ ndiponso masautso ndi nthawi zovuta zikadzakugwerani.+