Miyambo 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Njira zake n’zobweretsa chisangalalo ndipo misewu yake yonse ndi yamtendere.+