Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:27 Nsanja ya Olonda,10/15/2010, tsa. 151/15/2000, tsa. 2612/15/1993, ptsa. 20-21
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+