Miyambo 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Usanene kwa mnzako kuti, “Pita, ukabwerenso mawa ndidzakupatsa,” pamene uli ndi chinachake choti ungam’patse.+
28 Usanene kwa mnzako kuti, “Pita, ukabwerenso mawa ndidzakupatsa,” pamene uli ndi chinachake choti ungam’patse.+