Miyambo 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wokonda malangizo* amakondanso kudziwa zinthu,+ koma wodana ndi chidzudzulo ndi wopanda nzeru.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:1 Nsanja ya Olonda,1/15/2003, ptsa. 28-29